Skip to content

Vuto Ndichani

Popularity ยท Low

YouTube

Searching YouTube...

Lyrics

It's that money making music Ndalama zikandiyanja sindimasowa Ndimapenga nazo, ndimapenga nazo Ndalama zikandiyanja sindimasowa Ndimapenga nazo, ndimapenga nazo Tandigwile, tandigwile, happiness mbwe mbwe mbwe Tandigwile, tandigwile ine, happiness mbwe mbwe mbwe Tandigwile, tandigwile, happiness mbwe mbwe mbwe Happiness mbwe mbwe mbwe, happiness mbwe mbwe mbwe Tandigwile, tandigwile, happiness mbwe mbwe mbwe Tandigwile, tandigwile ine, happiness mbwe mbwe mbwe Tandigwile, tandigwile, happiness mbwe mbwe mbwe Happiness mbwe mbwe mbwe, happiness mbwe mbwe mbwe Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Vuto ndichani, ndalama zanga, kumandinena tandiuzeni Vuto ndichani, ndalama zanga, kumandinena tandiuzeni Vuto ndichani, ndalama zanga, kumandinena tandiuzeni Vuto ndichani, ndalama zanga, kumandinena tandiuzeni Iiiiiiiih iiiiiyaaaa hiii hiii Iiiiiiiih yaaaa hiiiiiyaa ah Iiiiiiiih iiiiiyaaaa iiiya iyaaa ah hii hii hii hii Iiiiiiiih iiiiiyaaaa iiiyaaaa aaa aaaah Anthu otani mumakondwela Zikamavuta mumakondwela Basi nkhani kundipekela, mwati uyu sizimuyendela Anthu otani mumakondwela Zikamavuta mumakondwela Basi nkhani kundipekela, mwati uyu sizimuyendela Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Zochepa ndili nazo zimandikwanila Anthu otani mumakondwela Zikamavuta mumakondwela Basi nkhani kundipekela, mwati uyu sizimuyendela Anthu otani mumakondwela Zikamavuta mumakondwela Basi nkhani kundipekela, mwati uyu sizimuyendela