Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Ngamila
Baaba Maal and Mumford & Sons and The Very Best
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Umafuna nthawi zonse
Uvutike moyo wonse
Kufuna zonse zabwino
Zikhale zako
Ufunefune bwanji
Sungalikwanitse dzikoli
Mapeto ake ndikunenetsa
Udzagonje ndiwe
You search all your life
Stealing all you find
And you stare at your own hands
Not the hands they entwine
Pokuti upeze chuma
Mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi
Kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi
Ngamila yanga ili kuti?
Chonsecho wakwera
Ngati wachitila dala
ย
Pokuti upeze chuma
Mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi
Kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi
Ngamila yanga ili kuti?
Chonsecho wakwera
Ngati wachitila dala
ย
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
Ngamila yanga ili kuti?
ย