Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Ulemelero Wanu
Free Worship Malawi
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
Listen
YouTube
1
2
3
0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi nchito ya manja anu
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi nchito ya manja anu
Ine ndiza
Kuimbirani
Ndikadari ndi moyo
Ndizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ine ndiza
Kuimbirani
Ndikadari ndi moyo
Ndizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani (oh)
Ndi nchito ya manja anu
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi chito ya manja anu
Oh ife Tiza
Kuimbirani
Tikandari ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ife Tiza
Kuimbirani
Tikandari ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ndipo Mulungu
Agate
Agate
Agate Agate
Mulungu agate
Salepela zoana
Iye Mulungu
Agate
Agate
Agate agate
Mulungu agate
Salepela zoana
Kodi ndiye
Alefa omega
Oyamba osiliza
Wachimpulumuso cha moyo wanga
Oh Iye mulungu
Agate
Agate
Agate agate
Mulungu agate
Salepela zoana
Iye ndiye
Alefa omega
Oyamba osiliza
Wachimpulumuso cha moyo wanga
Oh Iye mulungu
Agate
Agate
Agate agate
Mulungu agate
Salepela zoana
M'nalenga munthu
M'chifaniziro chanu
Ambuye
Kondwelani ndi nchito
Ya manja anu
M'nalenga munthu
M'chifaniziro chanu
Ambuye
Kondwelani ndi nchito
Ya manja anu
Ife Tiza
Kuimbirani
Tikandari ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wanta onse
Ife Tiza
Kuimbirani
Tikandari ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
ย