Skip to content

Cardio

Trappybeats.
Popularity ยท Low

YouTube

Searching YouTube...

Lyrics

Ngini Ili Sharp Taphusha Ndi boys yanga ija tikalinka Timaichemesa ife tikafika Timasiya nkhani ife tikadusa Ngini Ili Sharp Taphusha Ndi boys yanga ija tikalinka Timaichemesa ife tikafika Timaichemesa ife tikafika Tikupanga Udolo Boys yamenya call Tatipeze chapa Chanco Tagwetsa Kale Mabotolo Folo Tikupanga Udolo Boys yamenya call Tatipeze chapa Chanco Tagwetsa Kale Mabotolo Folo Tikuphusha Ngini Khala Ngati Cardio Tikusuntha Trynna Get Money Ngati Sadio On another level Nyimbo zathu munvela pa radio Cerebrity Status, Ma hater Outside Ali Panja Koma Tikangofika Pachema Pachema Koma Tikangofika Patentha Patentha Koma Tikangofika Pachema Pachema Koma Tikangofika Patentha Patentha