Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Stacey
Lucius Banda
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
I've chasing for you
But you've been running away
And when I think about you
Baby we're meant to be
I've been saying I love you
You've been saying you don't
But when I look in your eyes
Something is saying you do
Stacey, Stacey
Ndiwe mfumukazi yanga
Chikondi ngati cha bulangete
Chopita limodzi kumanda
Ndikudziwa kuti udzandilora
Mtima ukadzatsika
Ndakhumudwitsidwa kwambiri ih
Ukaona mamuna aliyense
Ndidziwa uli ndi mantha
Poti poyamba zimakoma eh
Ukumati amuna ndi agalu
Ukaganizira uja
Tapeza wina udzadabwa ah
Mmmh love will find a way
Love will find a way
If not tomorrow, the next day
Love will find a way
Mmh ooh!, ooh!
Ndakhala ndikufunsira
Kwa dzaka zitatu Stacey
Wayesera amuna awiri
Onsewa adakuliza
Ndakhala ndikulira
Chauta thandizeni
Ngati ndi nkhope idanyasa
Mtimawu ngokongola
Stacey, Stacey
Ndiwe mfumukazi yanga
Chikondi ngati cha bulangete
Chopita limodzi kumanda
Ndikudziwa kuti udzandilora
Mtima ukadzatsika
Ndakhumudwitsidwa kwambiri ih
Ukaona mamuna aliyense
Ndidziwa uli ndi mantha
Poti poyamba zimakoma ah
Ukumati amuna ndi agalu
Ukaganizira ujayo
Peza wina udzadabwa oh
I know that love will find a way
Love will find a way
If not tomorrow, the next day
Love will find a way
Nkhondo oh, nkhondo no
Stacey, Stacey
Stacey, Stacey
Ndiwe mfumukazi yanga
Chikondi ngati cha bulangete
Chopita limodzi kumanda (Stacey)
Ndikudziwa kuti udzandilora (Stacey)
Mtima ukadzatsika (Stacey)
Ndakhumudwitsidwa kwambiri ih
Ukaona mamuna aliyense
Ndidziwa uli ndi mantha
Poti poyamba zimakoma ah (Stacey)
(Ukumati amuna ndi agalu)
(Ukaganizira ujayo)
ย