Skip to content

Holy Water

Popularity ยท Low

YouTube

Searching YouTube...

Lyrics

Yeah Alright Y'all ready know (Kumaloto) (Siwe wakumaloto mwina) (Kumaloto) (Siwe (Tricky Beats ooo) wakumaloto mwina) Mchere ayy Usasakanike ndi sugar Ngati uli pano kufuna kundiyesa Akupweteketsa wakutuma Ngati wabwera kuzandiyesa (yesa) Ngati wabwera kuzandiwerenga (werenga) Ngati wabwera kuzandiyesa (yesa) Ngati wabwera kuzandiwerenga (werenga) Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ine zachibwana sikweni kweni Magwa mu chikondi zeni zeni Ndipo ukabhowa undimva pain Nde usandivutitse pusitse I don't need bad energy in my life Ndimagwira magobo to survive If you wanna stay show Me love Ngati uzi gulugusha (Catch a bus) Mmh tafuma apapa Funa ndikonzeke tafuma apa Mmh Ndachi lapa Zachikondi Zi ndazilapa Good only vibes wanted out here Sindikonda za daily Giving me love and nasilira Mene mowa Chikondi Mene ndigwilire Mchere Usasakanike ndi sugar ooh Ngati uli pano kufuna kundiyesa Akupweteketsa wakutuma Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto) (Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto) (Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga Kumaloto siwe wakumaloto mwina Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ngati ufuna wina Undiwuze ndikhonzoke eh Zoti uzindizunza zimenezo zilekeke Mmh hm Ma plan ndimasanja ndekha eh Money ndimasaka ndekha eh Nde usabwere ndi zondisokoneza eh Ndikzakuthila Holy water Mchere Usasakanike ndi sugar mmh Ngati uli pano kufuna kundiyesa Akupweteketsa wakutuma Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto) (Siwe wakumaloto mwina) Ngati wabwera kuzandiwerenga Ngati wabwera kuzandiyesa (Kumaloto) (Siwe wakumaloto mwina) ngati wabwera kuzandiwerenga (Kumaloto siwe wakumaloto mwina) Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ngati wabwera kuzandiyesa Ngati wabwera kuzandiwerenga Ngati wabwera kuzandiyesa Ngati wabwera kuzandiwerenga Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water Ndikuthila Holy water