Kuno (Mom's Call)
Popularity ยท Low
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Call inabwela
Ati
โhello ukundimva? Ine amamiโ
Ine ndati hello Masteni
Ati
โndikale unaimba phone,
Ndati ndikupatse moni.
Uli bwanji mwananga?
Kodi kufumbi kuli bwanji mwananga?โ
Ine ndati ndili welo kuno
Amami ndili welo kuno
Inde pena zikuvuta kuno
Pena moyo ukushupa kuno
Ati
โkukula ndi choncho mwananga
Dziwa moyo ndi choncho mwananga
Kuti pena zimayenda
Pena zimavuta
Koma udzipemphera
Udzipemphera
Kumapemphera
Udzipempheraโ