Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Amai Inu
Lucius Banda
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Mulibe mtima wachikondi
Amai inu
Ndikapita ndi edzi
Ndi amai inu
Ndi chiyani mukufuna?
Amai inu
Kuti musangalare
Kodi mama inu
Chikhala wena mkanamayamika ah yeah
Achepelenji amuna achikondi ah yeah
Akazi anzanu akulira mama ah yeah
Muli ndi tsoka losasimbika wawa ah yeah
Mukanjoya-njoya akazi wanga mudzandipeza
Nkhani zomwe ndikumazimva zikundiliza
Ndinakutenga kumudzi uli wofatsa
Unali mkazi wa ulemu
Kodi watani?
Ine ndayesetsa kuonetsa chikondi changa
Ndinali munthu wovuta
Ndidasintha ine
Ku m'mawa ndikakusiya kuntchito kwanu
Mdamva kuti ukumachoka ndi amuna wena
Mulibe mtima wachikondi
Amai inu
Ndikapita ndi edzi
Ndi amai inu
Ndi chiyani mukufuna?
Amai inu
Kuti musangalare
Kodi mama inu
Chikhala wena mkanamayamika ah yeah
Achepelenji amuna achikondi ah yeah
Akazi anzanu akulira mama ah yeah
Muli ndi tsoka losasimbika wawa ah yeah
Mumavetsa inu chisoni
Masiku ano
Akazi atayilila mokhumudzitsa
Amakudyetsa mankhwala, ati upuse
Chilichonse chomwe anene udzingolora
Yeah-le-le ah ha
Ati kandisiye ku casino
Iwe kulora
Akakumana ndi dzibwenzi
Iwe ukugona
M'bambo wabwinobwino wazelezeka
Kuthandiza akwawo onse adamuletsa
Da-da adamuletsa
Da-da adamuletsa
Mulibe mtima wachikondi
Amai inu
Ndikapita ndi edzi
Ndi amai inu
Ndi chiyani mukufuna?
Amai inu
Kuti musangalare
Kodi mama inu
Chikhala wena mkanamayamika ah yeah
Achepelenji amuna achikondi ah yeah
Akazi anzanu akulira mama ah yeah
Muli ndi tsoka losasimbika wawa ah yeah
ย
Helele eeey huu!
Don't let me go again
Three, two, one
Mulibe mtima wachikondi
Amai inu
Ndikapita ndi edzi
Ndi amai inu
Ndi chiyani mukufuna?
Amai inu
Kuti musangalare
Kodi mama inu
Chikhala wena mkanamayamika ah yeah
Achepelenji amuna achikondi ah yeah
Akazi anzanu akulira mama ah yeah
Muli ndi tsoka losasimbika wawa ah yeah
ย