Sindikwatila
Fredokiss
Popularity ยท Low
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Ey uh
Es es es
Ha ha china Fredo ase, (ghetto gutter)
Achina Fredo ada
Achina Fredo ada
Sitikwatira ase
Sindikwatira ase
Sitikwatira ada
Sindikwatira ase
Chibwana ndimakana ada sindikwatira
Mukakwatirakwatira ine nde ndikhala otsirizira
Zomwe nduma checker ngati maso anamizira
Mkazi wa bhobho she's about to get married
Adyetsa kwa abwana ake, achikulire
And what she doesn't know he's about to get buried
Mfana sakujaja holy loss is getting married
But he is getting married at the same time buried
Ada awawa alinso ndi chick yofatsa
Imavaya ku church
Imakonda ku praiser bad
Imawafila bad
Komano ada awawa kudzikhebako sinkhani
Amakoka bad, kanginiso kali mu blood ada afuna amale
Zomwe zumachitika izizi ngati nza dala
Akazi a size yanga onse akudyetsa kwa madala
Akadyetsadyetsa afuna ine ndidye zotsala
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Frenzo wanga panopa ndi B-A
All of us is happy panopa asinthe
Bawa amamenya koma za akazi njee
Umaziwa yama B-A wagwira mu church
Wagwira chick yoti yinatapata mkubona
Inayendayenda panopa inabona
Afana ali mu church koma ada sakuona
Akwatira chaka chatha, chaka chatha
First baby boy iwe ndi HIV
Amfana sakumvetsa iwe HIV
M'mene ndimalowa m'banja nnali vinigo
I'm like kachikena ada
Here we go
Zomwe zumachitika inu mukavala mphete
Ada wawa anavaya masters kunja
Mkazi wawo kuno daily ku Mastang kuja
Apeza mfana wachimwenye dzina lake Bunjar
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina ifeyo ada ada sitikwatira
Zomwe zumachitikachitika suzifila
Ndionetseni mkazi oti mwina andifila
Ondifilafila koma osazifilafila
Opilira akhalale painkiller
Life yathu isakhale comedy or thriller
Ndikadzala mbewu zanga adzitha kuthilira
When i get broke asayang'aneso kwina
When i'm not there asayang'aneso wina
Or ndita loser she should see me as a winner
Who knows what she wants
Iwe samayankha mwina
Ndikafusa fuso yankho straight
Osati mwina
Akhale wo praiser odzisamalira
Owoneka bho wojuduka wosapesa
(Mmh achina fredo mpaka zonsezo ase)
Eeh basi nde sitimala ifeyo
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo simukwatira ase? njee man
Nanga ada simukwatira ada? mayazi
Nanga inuyo? njee man
Nanga awowo? njee man
Uh uh uh sitikwatira
Achina Fredo ada
Ghetto gutter entertainment
Ukuziwa kale heh
Nde mafana musanakwatire
Anthu amene mumathamangira kukwatiranu
Mumakhala kuti simuli ready iyayi
Enanuso mufuna mukwatire
Komano mumapezeka kuti inuyo simunazitcheke kaye iyayi
Osati mfana chufukwa choti kaya uli ndi ka money
Iwe chifwa choti basi ungoziona kuti wakula
Ka mkazi ndekuti basi iweyo ukwatire iyayi
Kukwatira mmakhala kuti inuyo mukupangana ndi Jah Jah
Osamangolwatira zachibwana iyayi
Yeah
Whatchu want
Ya achina Fredo ase
Ya achina Fredo ada
Ghetto gutter entertainment
Dear devils on the beat
B-F-B
Whatchu want uh