Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Yekha
Kineo Madness, Aidfest Madness
Popularity · Low
+
Original
0
0
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Kaya mukuti mamunayi ndi wagulu
Ali ndi ankazi chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Kaya mukuti nkaziyu ndi wagulu
Ali ndi amuna chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Yekha yekha yekha yekha (amabwera yekha)
Yekha yekha yekha yekha(amabwera yekha)
Uyu ndiwanga wanga wanga basi (ndasaina ndasaina basi)
Kaya mukuti mamuona kuti ndi wina
Koma akabwera ndiwanga basi
Anthu akaduka inu chaka chino muva mbembe
Akapasule inu chaka chino muva (mbembe)
Anthu akaduka chaka chino muva (mbembe)
Akapasule inu chaka chino muva (mbembe)
Kaya mukuti mamunayi ndi wagulu
Ali ndi ankazi chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Kaya mukuti nkaziyu ndi wagulu
Ali ndi amuna chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Yekha yekha amabwera yekha
Yekha yekha amabwera yekha
All no no no no no (oh no)
Musandiuze kuti nditaye uyuyu(aaah)
Taona m'mene akuonekela bwino
Ndinasakha kalekale uyuyu
Akakakokha kwa ine ndimakina
Ndatola joker mutisiye muchedwa Akakakokha kwa ine ndimakina
Ndatola joker mutisiye muchedwa
Kaya mukuti mamunayi ndi wagulu
Ali ndi ankazi chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Kaya mukuti nkaziyu ndi wagulu
Ali ndi amuna chimulu
Koma akamabwera kwathu (amabwera yekha)
Yekha yekha amabwera yekha
Yekha yekha amabwera yekha