TRUE LOVE
Popularity · Low
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
Oh no
Fumbi boy, (boy)
Baby forever I'm grateful (forever I'm grateful)
Okay, okay, one time, one time
Preload (savage on the beat, Njuchi)
What have you done to me?
What have I eaten?
Ndinkati ndinazisiya izi ine
Mkati vimaluma ivi
Tell me why I'm feeling this way?
Wamutani mwana wa eni?
Kwawo ankadya koma kunenepa uh-uh
Kwam'mutenga mwezi umodzi wayamba kusala
True love, oh no
True love, oh no
Chikondi chake chandipanikiza
Chikubwera chonse ngati sugar sichoyezetsa
True love, ooh-ooh!
True love, oh-noo!
Chifukwa cha iwe my lover, ndatha mtunda
Ooh-ooh
Ooh-ooh
Chifukwa cha iwe my lover, ndatha mtunda, (yeah!)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Chifukwa cha iwe my lover ndatha mtunda
Sin'nali chonchi ine
Adabwa ma frenzo wa
Moyo wa ubatchala sindikuwusowa
Game yagoma 2-0
Full tank gauge gear folo
Pa nseu traffic ikandigwira
Mwanyamula chani bambo?
Ndimati ooh-ooh
Ndamyamula true love
Ooh-ooh, ndamyamula true love
Quantum overloaded
Olo abweretse breathalyzer
Ndimati ooh-ooh ndalawako true love
Ooh-ooh ndalawako true love
Baby forever I'm grateful
Chifukwa cha iwe my lover, ndatha mtunda (ay-yeah)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Chifukwa cha iwe my lover, ndatha mtunda, (ay-yeah)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Ooh-ooh, (ay-yeah)
Chifukwa cha iwe, chifukwa cha iwe
Ndatha mtunda
Zimakoma chonchi? (eeh)
Oh, kani zimabheba chonchi? (eeh)
Nthawi yonseyi unali kuti iwe? (eeh)
Ndungofuna tidzikhala chonchi, (ndatha mtunda)
Oh, kani zimakoma chonchi? (eeh)
Oh, kani zimabheba chonchi? (eeh)
Nthawi yonseyi unali kuti iwe? (eeh)
Ndungofuna ndizikhala chonchi ine
Ooh-ooh ndanyamula true love (inde my love)
Ooh-ooh ndanyamula true love (inde my love)
Ooh-ooh ndalawalako true love, (chifukwa cha iwe)
Ooh-ooh ndalawalapo true love, (chifukwa cha iwe)
(Ndatha mtunda)
Ooh-ooh ndanyamula true love
Ooh-ooh ndanyamula true love
My baby forever I'm grateful, (ooh-ooh ndanyamula true love)
Chifukwa cha iwe, chifukwa cha iwe, (ndalawalako true love)
Ndatha mtunda
Ooh, ooh
Eyo Baxter
Moon rapper
One time, one time