Gu Gu Gu
Crispy Malawi
Popularity · Low
YouTube
Searching YouTube...
Lyrics
(Timothy Got the Fire beats no matter what it is)
(Ayo Landie)
Ukamva Gu! gu! Gu! Gu speaker yakwa neighbour
Gu! Gu! Gu! speaker yakwa neighbour
Gu Gu! Gu! speaker yakwa neighbour
Ukamva!
Slatt
Kwabwera smokey Ndi Themba
Samaona kuti lero ndi lolemba
Kungodya ma Zaza ntibu tangokweza
Playlist ya DJ neighbor suzayiloweza
Chotsa ti nyimbo tako faka Crispy ndi Krazy
Za alamu anu ukamufunse Celba ndi Zeze
Brainlock in the mix itsitse ikweze
Ndili ndi chi keys chi Jeff isokoneze
Kwathu kumveka Nyimbo
Kwa neighbour kumveka nyama
Chispeaker kukopa fanz amayesa ngati ma scammer
The way I do my dance ngati MC Hammer
Speaker tangokweza nde today mu runner
Ndikudya Ka loud sound ili low
Ayy
Tandipatse cow kuti ndivine ngati nyau
She send me little letter
She says she's getting better
I'm never under pressure
Chi speaker ndangokweza
Ukamva Gu! gu! Gu! Gu speaker yakwa neighbour
Gu! Gu! Gu! speaker yakwa neighbour
Gu Gu! Gu! speaker yakwa neighbour
Ukamva!
Speaker yakwa neighbour indiboola makutu
Kungochoka vep akut speaker ituluke
Ungodina next uwone akutulutse
Kuti Gu!Gu!Gu!Gu! Mpakana Kuche
Kukanika kubleya man
Ma window kutseka blaz
Azimayi kuchola dance,ma babe Ku twerka man
Muno ndimu hood mwanga wina andinyumwitse
Yesa zida phwanga uwone fanz ikuwukire
Neighbour ziphokoso
Ndi Yambisa nkhondo
Ndivaya Ku popo
Ndivaya konko
Neighbour ziphokoso
Yambisa nkhondo
Vaya Ku popo
Vaya konko
Ah speaker yakwa ikati isokosere
Imakhala full blast basi asokoneze
Ndichi ntibu makina chimphaso makoswe
Koma De-Fra basi ndiyi bongose
Daily kwa neighbour ngati kuli ma demo
Iwe kufa makutu ngati wasonkha ya memo
Neighbour samamva za munthu
Iyeyo ndi wa ghettoSpeaker yake inathawa nawo mazeno
Neighbour Neighbour umatiwonjeza
Neighbour Neighbour pajatu ndinalonjeza
Koma tangowona sound yako wayikweza
Neighbour Neighbour
Neighbour Neighbour suzatheka
Ndazuka chifukwa cha noise
Speaker yakwa neighbour imeneyo
Ingolongola wangokweza Zima 808
Wayamba chama quarter to
Pano ili past two
Ndikungomva gugugu wandisokoneza Mutu
Iwe Neighbour bwanji ukukweza sound Ngati ndi December
Wayamba kale kale kuthoka sukuleka
Sound ili loud ngati Zaza ndi kukhwemba
Umandijayila tsiku lina ndizakukwenya
Uzandimva ndikanena
Pano sumakhala wekha
Makufila ndiwe neighbour
Koma nzakutopela
Ndikabwera kupeza sound wakweza
Kuli ana akufuna kubleya
Speaker yakwa neighbour imandisokoneza peace
Zoti ndimableya ndangodzuka Ku roller spliff
Ti ana tingodabwa kodi Ali kut Sticx
Moto sungayake opanda iyeyo call him please
Ndinali Ku pharmacy kugula Kaye mazza
Themba Ali ndi sprite Crispy Ali ndi Zaza
Magetsi akathima neighbour Ali ndi generator
Zoma flexer ka Mwana kake amandiletsa
Koma boys sizamva ndili naye Ku corner
Eko Ka gram Kalitchetche ta roller
Kukonda Zima speaker ngati ma sister Ku culture
Nditha kukagona konko mpaka kukacha