Skip to content

Interlude

Crispy Malawi
Popularity ยท Low

YouTube

Searching YouTube...

Lyrics

(Cheo Meek hiihihi) You know Yeah Turn it up Malawian (Welcome back Blake) Mhu Rest in peace to Patricia All I ever wanted was a mic ndi chi mixer Pano ma gee akafuna feature ndimalipilitsa Ena ndimawawaza ena ndimawakwiyitsa Eh I love my girl kungoti Talandira ndi Eliza Nditha kutchola door just to get Bros inside Ndilipa pa mirror like hell yeah I'm that nigga We in the music business a Diddy Ndi achina Jigga Remember how started ngati za jokes Now we moving city to city kupanga ma show Money ipange flow, Tikhale bho bho Ndimakhala busy mami ndimatanganidwa Ndiku runner new wave Ku Malawi Nthangwanika Kuthamangitsa gist koma osathamangira Kuvutitsa pa stage ngati mfana woyitanira (Akwere Nawo ya M'town) Ha Rest in peace Fati Khaza[?] Ndikudziwa wa Hitter kale Stu Ndi achina Martse Nkhata Kuwonetsa action mafana omangobwata Kuwapatsa chochita ana oti amangokhala Huh Rest in peace to my feelings Ma babe osa pusher ine sindingakufileni Undipeza Ku Stu ine si mfana wa Ku DM Album on the Way ndipatse space eh clear (space) Rest in peace to Patricia All I ever wanted was a mic ndi chi mixer Pano ma gee akafuna feature ndimalipilitsa Ena ndimawawaza ena ndimawafilitsa (Achina yeah) (yeah Eliza) (Nditha kutchola door just to get Bros inside) (Kutchola chitseko) (Ndilipa pa mirror like hell yeah I'm that nigga) (We in the music business ngat Jigga) (Ndi achina SPE) (Cheo Meek hiihihi mhuu)