Skip to content

Oweruza

Popularity ยท Low

Listen

YouTube

0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced

Lyrics

Ngati ndi mapeto a dzikoli Ine ndiye ndafikapo Chomwe ndingapemphe iwe Usamvere za wanthu Ndikamakuuza kuti ndimakukonda Sinditha kumvetsa ine unapenga iwe Sizilephera zokhoma kuzunza moyo wanga Ndinatchera khutu ine Anene anene Ngati ndi mtera mwanawe Ndilibe nazo ntchito Palibe ndingaluze ine. Kukhala ndi iwe Tawugwira mtimawo Tawugwira mtimawo tawugwira mtimawo Ndikuuze zambiri Anzako aja akumayimba phone Tawugwira mtimawo ndikuuze zambiri Usadodome mwanawe ameneyu ndiwako Ndiwawuza dadie lero Ndikamakuuza kuti amakukonda Sinditha kumvetsa ine. Wapengadi iwe Pali anzako ambiri akulira limodzi Kuyambira let mwali ndi mbiri yakale Tandiuzeko mwanawe zachinsinsi chakochi Unapeza banji iwe bwezi lokonda Tawugwira mtimawo Tawugwira mtimawo tawugwira mtimawo Ndikuuze zambiri Anzako aja akumayimba phone Tawugwira mtimawo ndikuuze zambiri