Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Mtendere
Driemo Mw
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
Listen
YouTube
1
2
3
0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Mtima wanga umaimba
Everytime I see your face ka ngelo weh
Love yanga sizasila
Sili monga kendulo
You make my heart go like duduke
Every time you see me
Moteromo mmene umandikondela
Nikumveka mendulo
I don't need no special day
To make you feel you special
Poti kwa iwe ndi ine
Everyday is valentines
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe
Nditu baby you are my piece of mind
Mmani pangiso deka
Ambiri ama kaikira alole adziwe
Ndita kala wanje
Koma ndiwe nyenyezi yanga
Omwe azabwera mowala
Ncholinga ndisatire
You make me sing skubi dubi doo
Skubi dubi dubi doo
Dubi like the way I do
Saza mwalile
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe
I don't wanna lose you
I don't wanna hurt you, no
I just wanna see you smilling
(I just wanna see you smiling)
Ndiwe mtendere wanga
Chimwemwe changa ndiwe
Zonse zanga ziimbila iwe
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe
Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh
Umaninvesa chimwemwe changa ndiwe, yeah
(Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh)
(Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe)
(Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh)
(Umaninvesa chimwemwe changa ndiwe, yeah)
ย