Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Sikoyamba
Afana Ceez
Popularity · Low
+
Original
0
0
Listen
YouTube
1
2
3
0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Sikoyamba kuduka aka
(Zati chani apa)
Aye yeyeyeyeye aye ish
Shasha
Iweyo ndi nzanga sindingakupangile nsanje
Timatipulua limodzi Monday mpakana Sunday
Iwe ngati uli nkati naneso ndili nkati
Ndiyeno lero ngati tazipeza nzanga tizipepese
Sikoyamba aka (Maluzi wa)
Sikoyamba aka (Kuduka ku)
Sikoyamba aka (Tizipepese)
Sikoyamba aka (Nzanga tizipezaso)
Sikoyamba aka (Maluziwa)
Sikoyamba aka
Sikoyamba aka
Sikoyamba aka
Inu malume sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka aka
Zati bwanji apa
Sopano
Uli ndi zinga?
Sikoyamba kuduka aka
Tizipepese
Mmmh
Landlord yake tampasa
Fridge nayo yadzadza
Bill mpakana mwezi wa mawa
Nzanga zonse tapanga
Landlord yake tampasa
Fridge nayo yadzadza
Bill mpakana mwezi wa mawa
Zonse tapanga
Tsono madala, apa tazipezaso
Ganyu tagwila, pano tizipepese
Ah madala, apa tazipezaso
Ganyu tagwila, pano tizipepese
Inu malume sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka
Ndalama zipite
Moyo usale
Tisangalale
Sikoyamba kuduka aka
Zati bwanji apa
Sopano
Uli ndi zinga?
Sikoyamba kuduka aka
Tizipepese
Sikuyamba kuduka aka