Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Bwanji
Suffix
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
Listen
YouTube
1
2
3
0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Ndi ulendo wautali uwu
Kaya tikafikako bwanji kaya
Ati kuli mvula ziphaliwali
Kaya ifeyo ka tikalimba
When we're married and we have a child
Does it mean she will love me less?
I am tryna figure it out
Will she care for my happiness?
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji? yeah
Na na na na na yeah
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
A couple of years a boy is growing old now
Wrestling to put my life in order
Nkhawa ndikamva zama divorce
Momwe akuchulukira mu church kuposa mabodza
Ma banja achitsanzo pano akusowa
Ati akazi a church nanji achikunja bola
Chikwati, changa kuza spender man zi dollar
Mkazi kuzandi player so kungobetsapo lobola
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji? yeah
Na na na na na yeah
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
A couple of years a boy is growing old now
Wrestling to put my life in order
Ma blander ndikupanga ndili mfanawa
Mkazalowa mu banja mwati sazandilondora?
They say the single you'll be to your boy i'm scared
Tidzakwanitsa kukhala two men i swear
Social media ikayamba kubatcher
Zama banja achikhristu omwe akungo player-wa ine mantha eh
Glory means i'm looking for an eaz before the fall
Ndimayiwalanso nane ndili ndizi fall
God, God please don't let me fall
For ma looks okha ndikonzeni character
I wanna wanna be a lion king for her not a cheater
Nzakhulupilira ngati ndiku cheater
I know God is bigger than my mistakes
Angazandipatse grace kuti nzakhake mfana okhulupilika
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Zimakhala bwanji? yeah
Na na na na na yeah
Zimakhala bwanji?
I wanna know right now
I wanna know
Ndi ulendo wautali uwu
Kaya tikafikako bwanji kaya
Ati kuli mvula ziphaliwali
Kaya ifeyo ka tikalimba
ย