Skip to content
Lyric
Dive
Public playlists
My playlists
Search
Sign in
Za Iyeyo
Kelvin Sings
Popularity ยท Low
+
๐ฒ๐ผ Nyanja ยท Original
0
0
Listen
YouTube
1
2
3
0:00 / 0:00
Loading YouTube player...
Lyrics offset
Synced
Lyrics
Original
Translation
Bilingual
Yeah, yeah, yeah
Oh, na-na-na
Oh, na-na-na, yeah
Nah, oh, oh, yeah-yeah
Ndakumana naye chiphadzuwa, 'wa
Kukongola kwake ngati mngelo
Mayendedwe ake a m'nchiyero
Amapemphela kukada
Atseka maso nagwada
Baibulo lake kumanja
Chimodzimodzinso kukacha
Ati anagwa nchikondi
Ndi mamuna wa mtanda
Nde ngati ndifuna ndimvane naye
Machitidwe anga afane naye
Ndi mamuna wa mtanda (wa mtanda)
Mamuna wa mtandayo (wa mtandayo)
Nde ndilekelanji ine
Oh, na-na, didziwe zambiri
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Ayy, yeah
Oh
Oh, oh, oh
Yeah
Nde ndayamba ulendo oyenda ndi mtima, 'yenda ndi mtima
Cholinga changa nchoti ndikafike kuli yankho langa
Alaliki a ineyo adandifotokozera
Zamwana wa Mlunguyo
Ndinso malemba ndikawerenga
Ukulu wake undiphunzitsa kuzichepetsa ine
Pakuti njira yopita kwawo ndiyopapatiza iyeyo
Koma Yesu anazama pati? (Pati?)
Wandisiya pakamwa kakasi (kasi)
Ndifunisisa nkhale naye (phati) phati
Ine ndidziwe zambiri
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo, oh, yeah-yeah
Oh, oh, oh, yeah-yeah
Kodi a Yesu anazama pati?
Wandisiya pakamwa kakasi
Ndifunisisa nkhale naye phati-phati
Ine ndidziwe zambiri
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
Za iyeyo, za iyeyo
Za iyeyo, ooh, oh, oh (za iyeyo)
Ooh-ooh, oh, oh
ย